1 Akorinto 4:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma izi, abale, ndadziphiphiritsira ndekha ndi Apolo, cifukwa ca inu, kuti mwa ife mukaphunzire kusapitirira zimene zilembedwa; kuti pasakhale mmodzi wodzitukumulira mnzace ndi kukana wina.

1 Akorinto 4

1 Akorinto 4:3-11