1 Akorinto 2:15-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Koma iye amene ali wauzimu ayesa zonse, koma iye yekha sayesedwa ndi mmodzi yense.

16. Pakuti wadziwa ndani mtima wa Ambuye, kuti akamlangize iye? Koma ife tiri nao mtima wa Kristu.

1 Akorinto 2