1 Akorinto 15:44-47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

44. lifesedwa thupi Iacibadwidwe, liukitsidwa thupi lauzimu. Ngati pali thupi Iacibadwidwe, palinso lauzimu.

45. Koteronso kwalembedwa, 11 Munthu woyamba, Adamu, anakhala mzimu wamoyo. 12 Adamu wotsirizayo anakhala mzimu wakulenga moyo.

46. Koma cauzimu siciri coyamba, koma cacibadwidwe; pamenepo cauzimu.

47. 13 Munthu woyambayo ali wapansi, wanthaka. Munthu waciwiri ali wakumwamba.

1 Akorinto 15