1 Akorinto 12:20-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Kama tsopano pali ziwalo zambiri, kama thupi limodzi.

21. Ndipo dise silingathe kunena kwa dzanja, Sindikufuna iwe, kapenanso mutu kwa mapazi, Sindikufunani inu.

22. Koma makamakatu ziwalozo zoyesedwa zofoka m'thupi, zifunika;

23. ndipo zimene tiziyesa Zocepa ulemum'thupi, pa izi tiika ulemu wocuruka woposa; ndi zinthu zosakoma zikhala naco cokometsera coposa,

1 Akorinto 12