1 Akorinto 11:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanga mulibe nyumba za kudyeramo ndi kumweramo? Kapena kodi munyoza Eklesia wa Mulungu, ndi kunyoza iwo amene alibe kanthu? Ndidzanena ciani kwa inu? Kodi ndidzatama inu m'menemo? Sindikutamani.

1 Akorinto 11

1 Akorinto 11:12-29